Yobu 6:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mundilangize, ndipo ine ndikhala chete.+Zimene ndalakwitsa, mundidziwitse.+