-
Yobu 42:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Tsopano utenge ng’ombe zamphongo 7 ndi nkhosa zamphongo 7.+ Upite nazo kwa mtumiki wanga Yobu,+ ndipo inuyo mukadziperekere nsembe yopsereza. Ndiyeno Yobu mtumiki wanga akakupemphererani.+ Ine ndimvera iye yekhayo basi kuti ndisakuchititseni manyazi chifukwa cha zopusa zimene mwachita, popeza simunanene zoona za ine monga wachitira Yobu mtumiki wanga.”+
-