Salimo 56:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Popeza kuti ndine wogwirizana ndi Mulungu, ndidzatamanda mawu ake.+Ine ndimadalira Mulungu, sindidzaopa.+Kodi munthu angandichite chiyani?+
4 Popeza kuti ndine wogwirizana ndi Mulungu, ndidzatamanda mawu ake.+Ine ndimadalira Mulungu, sindidzaopa.+Kodi munthu angandichite chiyani?+