Salimo 102:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kuti amve kuusa moyo kwa akaidi,+Ndi kumasula anthu opita kukaphedwa.+