Mlaliki 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Zinthu zonse n’zotopetsa,+ ndipo palibe angazifotokoze. Diso silikhuta n’kuona,+ ndipo khutu silidzaza chifukwa cha kumva.+ Mlaliki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:8 Nsanja ya Olonda,11/1/2006, tsa. 13
8 Zinthu zonse n’zotopetsa,+ ndipo palibe angazifotokoze. Diso silikhuta n’kuona,+ ndipo khutu silidzaza chifukwa cha kumva.+