Mlaliki 7:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ineyo ndinaganiziranso mumtima mwanga+ kuti ndidziwe, ndifufuze, ndiponso ndifunefune nzeru.+ Ndinafunanso kudziwa zimene zimayambitsa zinthu,+ ndiponso kudziwa kuipa kwa kupusa ndi uchitsiru wa misala.+
25 Ineyo ndinaganiziranso mumtima mwanga+ kuti ndidziwe, ndifufuze, ndiponso ndifunefune nzeru.+ Ndinafunanso kudziwa zimene zimayambitsa zinthu,+ ndiponso kudziwa kuipa kwa kupusa ndi uchitsiru wa misala.+