Mlaliki 8:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma ngakhale zili choncho, ndaona anthu oipa akuikidwa m’manda.+ Ndaonanso mmene iwo anabwerera ndi mmene anachokera pamalo oyera,+ n’kuiwalika mumzinda umene anali kuchitiramo zoipazo.+ Izinso n’zachabechabe.
10 Koma ngakhale zili choncho, ndaona anthu oipa akuikidwa m’manda.+ Ndaonanso mmene iwo anabwerera ndi mmene anachokera pamalo oyera,+ n’kuiwalika mumzinda umene anali kuchitiramo zoipazo.+ Izinso n’zachabechabe.