Yesaya 17:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Masana ukhoza kuumangira mpanda wabwino munda wakowo, ndipo m’mawa ukhoza kuchititsa mbewu yako kuti iphuke. Koma zokolola zake zidzathawa m’tsiku la matenda ndi ululu wosachiritsika.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:11 Yesaya 1, ptsa. 196-197
11 Masana ukhoza kuumangira mpanda wabwino munda wakowo, ndipo m’mawa ukhoza kuchititsa mbewu yako kuti iphuke. Koma zokolola zake zidzathawa m’tsiku la matenda ndi ululu wosachiritsika.+