Yesaya 23:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mbewu za ku Sihori+ ndi zokolola za kumtsinje wa Nailo, zimene zinali kuyenda pamadzi ambiri ndiponso zimene zinali kukubweretserani ndalama, zakhala phindu la mitundu ina ya anthu.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:3 Yesaya 1, ptsa. 245-246
3 Mbewu za ku Sihori+ ndi zokolola za kumtsinje wa Nailo, zimene zinali kuyenda pamadzi ambiri ndiponso zimene zinali kukubweretserani ndalama, zakhala phindu la mitundu ina ya anthu.+