Yesaya 46:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ine sindisintha ngakhale kwa wokalamba,+ ndipo munthu wa imvi ndimamunyamula nthawi zonse.+ Ndithu ineyo ndidzachitapo kanthu+ kuti ndiwatenge, ndiwanyamule ndi kuwapulumutsa.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 46:4 Yesaya 2, tsa. 97
4 Ine sindisintha ngakhale kwa wokalamba,+ ndipo munthu wa imvi ndimamunyamula nthawi zonse.+ Ndithu ineyo ndidzachitapo kanthu+ kuti ndiwatenge, ndiwanyamule ndi kuwapulumutsa.+