Yesaya 52:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Dzuka pafumbi pamene ulipo.+ Sansa fumbilo, khala pamalo aulemu iwe Yerusalemu. Masula zingwe zimene zili m’khosi mwako, iwe mwana wamkazi wa Ziyoni wogwidwa ndi kutengedwa kupita kudziko lina.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 52:2 Yesaya 2, ptsa. 180-182
2 Dzuka pafumbi pamene ulipo.+ Sansa fumbilo, khala pamalo aulemu iwe Yerusalemu. Masula zingwe zimene zili m’khosi mwako, iwe mwana wamkazi wa Ziyoni wogwidwa ndi kutengedwa kupita kudziko lina.+