Yesaya 64:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Inu Yehova musatikwiyire kwambiri,+ ndipo musakumbukire zolakwa zathu kwamuyaya.+ Chonde, kumbukirani kuti tonsefe ndife anthu anu.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 64:9 Yesaya 2, tsa. 368
9 Inu Yehova musatikwiyire kwambiri,+ ndipo musakumbukire zolakwa zathu kwamuyaya.+ Chonde, kumbukirani kuti tonsefe ndife anthu anu.+