Yeremiya 38:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndiyeno Ebedi-meleki Mwitiyopiya anauza Yeremiya kuti: “Kulunga zingwezo ndi nsanza komanso ndi zidutswa za nsalu ndipo uziike m’khwapa.” Yeremiya anachitadi zomwezo.+
12 Ndiyeno Ebedi-meleki Mwitiyopiya anauza Yeremiya kuti: “Kulunga zingwezo ndi nsanza komanso ndi zidutswa za nsalu ndipo uziike m’khwapa.” Yeremiya anachitadi zomwezo.+