Ezekieli 11:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Choncho uwauze kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ndidzakusonkhanitsani kuchokera kwa anthu a mitundu yosiyanasiyana ndiponso kuchokera m’mayiko amene ndinakubalalitsirani, ndipo ndidzakupatsani dziko la Isiraeli.”+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:17 Nsanja ya Olonda,5/1/1997, ptsa. 19-209/15/1988, tsa. 15
17 “Choncho uwauze kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ndidzakusonkhanitsani kuchokera kwa anthu a mitundu yosiyanasiyana ndiponso kuchokera m’mayiko amene ndinakubalalitsirani, ndipo ndidzakupatsani dziko la Isiraeli.”+