Ezekieli 16:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Iwe sikuti unangoyenda chabe m’njira zawo ndiponso sikuti unangochita zinthu motsatira zinthu zawo zonyansa,+ koma m’nthawi yochepa unayamba kuchita zinthu zoipa kwambiri kuposa iwowo m’njira zako zonse.+
47 Iwe sikuti unangoyenda chabe m’njira zawo ndiponso sikuti unangochita zinthu motsatira zinthu zawo zonyansa,+ koma m’nthawi yochepa unayamba kuchita zinthu zoipa kwambiri kuposa iwowo m’njira zako zonse.+