Ezekieli 36:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pamenepo iwo anapita kwa anthu a mitundu ina ndipo anthuwo anayamba kudetsa dzina langa loyera+ ponena za iwowo kuti, ‘Awa ndi anthu a Yehova, ndipo anachoka m’dziko lake.’+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 36:20 Nsanja ya Olonda,9/15/1988, tsa. 24
20 Pamenepo iwo anapita kwa anthu a mitundu ina ndipo anthuwo anayamba kudetsa dzina langa loyera+ ponena za iwowo kuti, ‘Awa ndi anthu a Yehova, ndipo anachoka m’dziko lake.’+