Ezekieli 37:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Koma iwe mwana wa munthu, tenga ndodo+ ndi kulembapo kuti, ‘Ndodo ya Yuda ndi anzake, ana a Isiraeli.’+ Utengenso ndodo ina ndi kulembapo kuti, ‘Ndodo ya Yosefe yoimira Efuraimu+ komanso anzawo onse a nyumba ya Isiraeli.’+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 37:16 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),1/2022, tsa. 22 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),1/2018, tsa. 14 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),7/2016, ptsa. 31-32 Nsanja ya Olonda,9/15/1988, tsa. 25
16 “Koma iwe mwana wa munthu, tenga ndodo+ ndi kulembapo kuti, ‘Ndodo ya Yuda ndi anzake, ana a Isiraeli.’+ Utengenso ndodo ina ndi kulembapo kuti, ‘Ndodo ya Yosefe yoimira Efuraimu+ komanso anzawo onse a nyumba ya Isiraeli.’+
37:16 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),1/2022, tsa. 22 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),1/2018, tsa. 14 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),7/2016, ptsa. 31-32 Nsanja ya Olonda,9/15/1988, tsa. 25