5 Tsopano Yehova anandiuza kuti: “Iwe mwana wa munthu, khala tcheru+ ndipo uone ndi maso ako. Umve ndi makutu ako zonse zimene ndikukuuza zokhudza malangizo ndi malamulo onse a nyumba ya Yehova. Uonetsetse khomo la Nyumbayi ndi zipata zonse zotulukira m’malo opatulikawa.