Ezekieli 47:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno munthu uja anapita mbali ya kum’mawa atatenga chingwe choyezera m’manja mwake.+ Kenako anayeza mtsinjewo mikono 1,000 kuchokera pa Nyumba ija, ndipo anandiuza kuti ndiwoloke mtsinjewo. Madziwo anali olekeza m’mapazi.
3 Ndiyeno munthu uja anapita mbali ya kum’mawa atatenga chingwe choyezera m’manja mwake.+ Kenako anayeza mtsinjewo mikono 1,000 kuchokera pa Nyumba ija, ndipo anandiuza kuti ndiwoloke mtsinjewo. Madziwo anali olekeza m’mapazi.