Danieli 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma mukandiuza malotowo ndi kuwamasulira, ine ndikupatsani mphatso, mphoto ndi ulemerero wochuluka.+ Choncho ndiuzeni malotowo ndipo muwamasulire.”
6 Koma mukandiuza malotowo ndi kuwamasulira, ine ndikupatsani mphatso, mphoto ndi ulemerero wochuluka.+ Choncho ndiuzeni malotowo ndipo muwamasulire.”