Danieli 2:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Munapitiriza kuchiyang’ana kufikira mwala unadulidwa kuphiri koma osati ndi manja a munthu.+ Mwalawo unamenya chifanizirocho kumapazi ake achitsulo chosakanizika ndi dongo ndipo unawapera.+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:34 Ulosi wa Danieli, ptsa. 60-62 Galamukani!,1/8/1991, tsa. 29 Nsanja ya Olonda,11/15/1986, tsa. 7
34 Munapitiriza kuchiyang’ana kufikira mwala unadulidwa kuphiri koma osati ndi manja a munthu.+ Mwalawo unamenya chifanizirocho kumapazi ake achitsulo chosakanizika ndi dongo ndipo unawapera.+