35 Pamenepo chitsulo, dongo, mkuwa, siliva ndi golide, zonsezi zinaphwanyikaphwanyika ndipo zinakhala ngati mankhusu apamalo opunthirapo mbewu+ m’chilimwe. Mphepo inaziuluza moti sizinaonekenso.+ Koma mwala umene unamenya chifanizirocho unakhala phiri lalikulu ndipo linadzaza dziko lonse lapansi.+