Danieli 9:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Tsopano inu Mulungu wathu, imvani pemphero la mtumiki wanu ndi kuchonderera kwake. Malo anu opatulika amene awonongedwa+ akomereni mtima,+ inu Yehova, chifukwa cha dzina lanu.
17 Tsopano inu Mulungu wathu, imvani pemphero la mtumiki wanu ndi kuchonderera kwake. Malo anu opatulika amene awonongedwa+ akomereni mtima,+ inu Yehova, chifukwa cha dzina lanu.