Numeri 6:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Yehova akukomereni mtima,+ ndipo akuyanjeni.+ Salimo 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pali ambiri amene akunena kuti: “Ndani adzationetsa zinthu zabwino?”Inu Yehova, tiunikeni ndi kuwala kwa nkhope yanu.+ Salimo 67:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 67 Mulungu adzatiyanja ndi kutidalitsa.+Iye adzatikomera mtima,+ [Seʹlah.]
6 Pali ambiri amene akunena kuti: “Ndani adzationetsa zinthu zabwino?”Inu Yehova, tiunikeni ndi kuwala kwa nkhope yanu.+