Hoseya 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako ana a Isiraeli adzabwerera ndi kufunafuna Yehova Mulungu wawo+ ndiponso Davide mfumu yawo.+ Iwo adzabwera kwa Yehova akunjenjemera+ ndipo adzafunafuna ubwino wake m’masiku otsiriza.+ Hoseya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:5 Nsanja ya Olonda,8/15/1991, tsa. 17
5 Kenako ana a Isiraeli adzabwerera ndi kufunafuna Yehova Mulungu wawo+ ndiponso Davide mfumu yawo.+ Iwo adzabwera kwa Yehova akunjenjemera+ ndipo adzafunafuna ubwino wake m’masiku otsiriza.+