Yeremiya 30:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Inu mudzatumikira Yehova Mulungu wanu ndi Davide mfumu yanu+ imene ndidzakuutsirani.”+ Ezekieli 34:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndidzazipatsa m’busa mmodzi,+ amene ndi mtumiki wanga Davide,+ ndipo adzazidyetsa. Iye adzakhala m’busa wawo ndipo adzazidyetsadi.+ Ezekieli 37:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndidzawaphatikiza kuti akhale mtundu umodzi m’dzikolo,+ m’mapiri a Isiraeli. Onsewo adzakhala ndi mfumu imodzi+ ndipo sadzakhalanso mitundu iwiri kapena kugawanika kukhala maufumu awiri.+ Amosi 9:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “‘Pa tsiku limenelo, ndidzautsa+ nyumba+ ya Davide imene inagwa,+ ndi kukonza mmene khoma* lake linawonongeka. Ndidzautsa mabwinja ake ndipo ndidzaimanga kuti ikhale ngati masiku akale.+ Luka 1:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ameneyu adzakhala wamkulu+ ndipo adzatchedwa Mwana wa Wam’mwambamwamba.+ Yehova Mulungu adzam’patsa mpando wachifumu+ wa Davide atate wake.+ Chivumbulutso 22:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “‘Ine Yesu, ndinatumiza mngelo wanga kudzachitira umboni zinthu izi kwa inu, kuti zithandize mipingo. Ine ndine muzu+ ndi mbadwa+ ya Davide. Ndinenso nthanda yonyezimira.’”+
23 Ndidzazipatsa m’busa mmodzi,+ amene ndi mtumiki wanga Davide,+ ndipo adzazidyetsa. Iye adzakhala m’busa wawo ndipo adzazidyetsadi.+
22 Ndidzawaphatikiza kuti akhale mtundu umodzi m’dzikolo,+ m’mapiri a Isiraeli. Onsewo adzakhala ndi mfumu imodzi+ ndipo sadzakhalanso mitundu iwiri kapena kugawanika kukhala maufumu awiri.+
11 “‘Pa tsiku limenelo, ndidzautsa+ nyumba+ ya Davide imene inagwa,+ ndi kukonza mmene khoma* lake linawonongeka. Ndidzautsa mabwinja ake ndipo ndidzaimanga kuti ikhale ngati masiku akale.+
32 Ameneyu adzakhala wamkulu+ ndipo adzatchedwa Mwana wa Wam’mwambamwamba.+ Yehova Mulungu adzam’patsa mpando wachifumu+ wa Davide atate wake.+
16 “‘Ine Yesu, ndinatumiza mngelo wanga kudzachitira umboni zinthu izi kwa inu, kuti zithandize mipingo. Ine ndine muzu+ ndi mbadwa+ ya Davide. Ndinenso nthanda yonyezimira.’”+