Amosi 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Yehova wanena kuti, ‘“Popeza kuti Mowabu+ anapanduka mobwerezabwereza, sindidzamusinthira chigamulo changa. Sindidzamusinthira chigamulocho chifukwa chakuti anatentha mafupa a mfumu ya Edomu kuti apeze laimu.+
2 “Yehova wanena kuti, ‘“Popeza kuti Mowabu+ anapanduka mobwerezabwereza, sindidzamusinthira chigamulo changa. Sindidzamusinthira chigamulocho chifukwa chakuti anatentha mafupa a mfumu ya Edomu kuti apeze laimu.+