12 “Yehova wanena kuti, ‘Monga mmene m’busa amapulumutsira ziboda ziwiri za chiweto ndi kachidutswa ka khutu m’kamwa mwa mkango,+ nawonso ana a Isiraeli amene akukhala m’Samariya pamipando yapamwamba+ ndi kugona pamabedi a ku Damasiko+ adzapulumuka ochepa chabe m’manja mwa adani awo.’