Nahumu 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yehova sakwiya msanga+ ndipo ali ndi mphamvu zambiri,+ komatu Yehova salephera kulanga wolakwa.+ Njira yake ili mumphepo yowononga ndi mumphepo yamkuntho. Mitambo ndilo fumbi lopondapo mapazi ake.+ Nahumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:3 Yandikirani, tsa. 45 Nsanja ya Olonda,11/1/2001, ptsa. 8-9
3 Yehova sakwiya msanga+ ndipo ali ndi mphamvu zambiri,+ komatu Yehova salephera kulanga wolakwa.+ Njira yake ili mumphepo yowononga ndi mumphepo yamkuntho. Mitambo ndilo fumbi lopondapo mapazi ake.+