Mateyu 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Samalani kuti musamachite chilungamo chanu+ pamaso pa anthu ndi cholinga chakuti akuoneni, chifukwa mukatero simudzalandira mphoto kwa Atate wanu amene ali kumwamba. Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:1 Nsanja ya Olonda,2/15/2009, ptsa. 13-1410/1/1990, ptsa. 15-16
6 “Samalani kuti musamachite chilungamo chanu+ pamaso pa anthu ndi cholinga chakuti akuoneni, chifukwa mukatero simudzalandira mphoto kwa Atate wanu amene ali kumwamba.