Mateyu 8:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma Yesu anamuyankha kuti: “Nkhandwe zili ndi mapanga ndipo mbalame zam’mlengalenga zili ndi zisa, koma Mwana wa munthu alibiretu poti n’kutsamira mutu wake.”+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:20 Yandikirani, tsa. 291 Yesu—Ndi Njira, ptsa. 154-155 Nsanja ya Olonda,11/15/2011, tsa. 243/15/1988, tsa. 24
20 Koma Yesu anamuyankha kuti: “Nkhandwe zili ndi mapanga ndipo mbalame zam’mlengalenga zili ndi zisa, koma Mwana wa munthu alibiretu poti n’kutsamira mutu wake.”+
8:20 Yandikirani, tsa. 291 Yesu—Ndi Njira, ptsa. 154-155 Nsanja ya Olonda,11/15/2011, tsa. 243/15/1988, tsa. 24