Mateyu 10:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Amene walandira mneneri chifukwa ndi mneneri adzalandira mphoto yofanana ndi imene mneneri amalandira,+ ndipo amene walandira munthu wolungama chifukwa ndi wolungama adzalandira mphoto yofanana ndi imene munthu wolungama amalandira.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:41 Nsanja ya Olonda,11/1/2003, tsa. 12
41 Amene walandira mneneri chifukwa ndi mneneri adzalandira mphoto yofanana ndi imene mneneri amalandira,+ ndipo amene walandira munthu wolungama chifukwa ndi wolungama adzalandira mphoto yofanana ndi imene munthu wolungama amalandira.+