Mateyu 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pa nthawi ina, Yesu anali kudutsa m’munda wa tirigu pa tsiku la sabata.+ Ophunzira ake anamva njala ndipo anayamba kubudula ngala za tirigu n’kumadya.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:1 Yesu—Ndi Njira, tsa. 76 Nsanja ya Olonda,11/15/1997, tsa. 281/15/1987, tsa. 22
12 Pa nthawi ina, Yesu anali kudutsa m’munda wa tirigu pa tsiku la sabata.+ Ophunzira ake anamva njala ndipo anayamba kubudula ngala za tirigu n’kumadya.+