Maliko 8:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Iye anagwira dzanja la munthu wakhunguyo, ndi kupita naye kunja kwa mudzi. Kumeneko iye analavulira+ m’maso mwake, ndi kuika manja ake pa munthuyo ndi kumufunsa kuti: “Kodi ukuona chilichonse?” Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:23 “Wotsatira Wanga,” tsa. 154 Nsanja ya Olonda,4/15/2008, tsa. 294/1/2008, tsa. 302/15/2008, tsa. 292/15/2000, tsa. 17
23 Iye anagwira dzanja la munthu wakhunguyo, ndi kupita naye kunja kwa mudzi. Kumeneko iye analavulira+ m’maso mwake, ndi kuika manja ake pa munthuyo ndi kumufunsa kuti: “Kodi ukuona chilichonse?”
8:23 “Wotsatira Wanga,” tsa. 154 Nsanja ya Olonda,4/15/2008, tsa. 294/1/2008, tsa. 302/15/2008, tsa. 292/15/2000, tsa. 17