Maliko 13:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Pakuti mtundu udzaukirana ndi mtundu wina, ndiponso ufumu ndi ufumu wina.+ Kudzakhala zivomezi+ m’malo osiyanasiyana ndiponso kudzakhala njala.+ Zimenezi ndi chiyambi cha masautso, ngati mmene zimayambira zowawa za pobereka.+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:8 Nsanja ya Olonda,5/1/2011, tsa. 53/15/2008, tsa. 1210/15/1988, tsa. 3
8 “Pakuti mtundu udzaukirana ndi mtundu wina, ndiponso ufumu ndi ufumu wina.+ Kudzakhala zivomezi+ m’malo osiyanasiyana ndiponso kudzakhala njala.+ Zimenezi ndi chiyambi cha masautso, ngati mmene zimayambira zowawa za pobereka.+