Maliko 15:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Ndiyeno Yosefe anagula nsalu yabwino kwambiri ndi kumutsitsa. Atatero anamukulunga ndi nsalu yabwino kwambiri ija ndi kumuika+ m’manda+ amene anawasema m’thanthwe. Anagubuduza chimwala ndi kutseka pakhomo la manda achikumbutsowo.+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:46 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),10/2017, tsa. 20 Nsanja ya Olonda,3/1/2013, tsa. 8
46 Ndiyeno Yosefe anagula nsalu yabwino kwambiri ndi kumutsitsa. Atatero anamukulunga ndi nsalu yabwino kwambiri ija ndi kumuika+ m’manda+ amene anawasema m’thanthwe. Anagubuduza chimwala ndi kutseka pakhomo la manda achikumbutsowo.+