Luka 6:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 “Koma inu amene mukumvetseranu ine ndikukuuzani kuti, Pitirizani kukonda adani anu+ ndi kuchita zabwino+ kwa amene akudana nanu. Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:27 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, article 195 Nsanja ya Olonda,5/15/2008, tsa. 8
27 “Koma inu amene mukumvetseranu ine ndikukuuzani kuti, Pitirizani kukonda adani anu+ ndi kuchita zabwino+ kwa amene akudana nanu.