Luka 22:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Atachoka kumeneko anapita kuphiri la Maolivi monga anali kuchitira nthawi zonse. Ophunzira nawonso anamutsatira.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:39 Yesu—Ndi Njira, tsa. 282 Nsanja ya Olonda,3/1/1989, tsa. 17
39 Atachoka kumeneko anapita kuphiri la Maolivi monga anali kuchitira nthawi zonse. Ophunzira nawonso anamutsatira.+