Luka 23:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Herode ataona Yesu anakondwera kwambiri, chifukwa kwa nthawi yaitali ndithu anali kufunitsitsa kuti amuone+ popeza anali kumva+ za iye. Komanso anali kuyembekezera kuona chizindikiro chimene iye angachite. Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:8 Yesu—Ndi Njira, tsa. 292 Nsanja ya Olonda,12/15/1990, tsa. 8
8 Herode ataona Yesu anakondwera kwambiri, chifukwa kwa nthawi yaitali ndithu anali kufunitsitsa kuti amuone+ popeza anali kumva+ za iye. Komanso anali kuyembekezera kuona chizindikiro chimene iye angachite.