37 Pamenepo Pilato anati: “Chabwino, koma kodi ndiwe mfumu?” Yesu anayankha kuti: “Mukunena nokha kuti ndine mfumu.+ Chimene ndinabadwira, ndiponso chimene ndinabwerera m’dziko, ndicho kudzachitira umboni choonadi.+ Aliyense amene ali kumbali ya choonadi+ amamvera mawu anga.”+