Yohane 20:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tsiku loyamba+ la mlunguwo, Mariya Mmagadala anabwera kumanda achikumbutsowo m’mawa kwambiri, kudakali mdima, ndipo anaona kuti mwala wachotsedwa kale pamanda achikumbutsowo.+
20 Tsiku loyamba+ la mlunguwo, Mariya Mmagadala anabwera kumanda achikumbutsowo m’mawa kwambiri, kudakali mdima, ndipo anaona kuti mwala wachotsedwa kale pamanda achikumbutsowo.+