Machitidwe 4:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Choncho atawonjezera kuwaopseza, anawamasula, pakuti sanapeze chifukwa chilichonse chowapatsira chilango. Komanso anaopa anthu,+ pakuti onse anali kutamanda Mulungu chifukwa cha zimene zinachitikazo.
21 Choncho atawonjezera kuwaopseza, anawamasula, pakuti sanapeze chifukwa chilichonse chowapatsira chilango. Komanso anaopa anthu,+ pakuti onse anali kutamanda Mulungu chifukwa cha zimene zinachitikazo.