Aroma 16:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Moni kwa Anduroniko ndi Yuniya, omwe ndi achibale anga+ ndi akaidi anzanga.+ Amenewa ndi amuna odziwika kwambiri kwa atumwi ndiponso akhala ogwirizana+ ndi Khristu kwa nthawi yaitali kuposa ine. Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:7 Nsanja ya Olonda,10/1/1988, tsa. 13
7 Moni kwa Anduroniko ndi Yuniya, omwe ndi achibale anga+ ndi akaidi anzanga.+ Amenewa ndi amuna odziwika kwambiri kwa atumwi ndiponso akhala ogwirizana+ ndi Khristu kwa nthawi yaitali kuposa ine.