6 Koma pa nthawi ino abale, ngati ineyo ndingabwere kwa inu ndikulankhula malilime, kodi mungapindulepo chiyani ngati sindingakulankhuleni ndi mawu amene ndalandira kuchokera kwa Mulungu,+ kapena ndi mphatso yodziwa zinthu,+ kapena ndi ulosi, kapena ndi chiphunzitso?