2 Akorinto 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti ngati malamulo olembedwa, amene anatha patapita nthawi, anaperekedwa ndi ulemerero,+ ndiye kuti okhalapo nthawi zonse adzakhala ndi ulemerero woposa pamenepo.+
11 Pakuti ngati malamulo olembedwa, amene anatha patapita nthawi, anaperekedwa ndi ulemerero,+ ndiye kuti okhalapo nthawi zonse adzakhala ndi ulemerero woposa pamenepo.+