Agalatiya 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndine wodabwa kuti mwapatutsidwa mwamsanga, kuchoka kwa Iye+ amene anakuitanani mwa kukoma mtima kwakukulu kwa Khristu,+ ndipo mwakopeka ndi uthenga wabwino wamtundu wina.+
6 Ndine wodabwa kuti mwapatutsidwa mwamsanga, kuchoka kwa Iye+ amene anakuitanani mwa kukoma mtima kwakukulu kwa Khristu,+ ndipo mwakopeka ndi uthenga wabwino wamtundu wina.+