20 Ndinapachikidwa limodzi ndi Khristu.+ Si inenso amene ndikukhala ndi moyo,+ koma Khristu ndi amene akukhala ndi moyo mwa ine.+ Zoonadi, moyo umene ndikukhala tsopano,+ ndikukhala mokhulupirira Mwana wa Mulungu, amene anandikonda ndi kudzipereka yekha chifukwa cha ine.+