Aefeso 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mwa kukoma mtima kwakukulu kumeneku, ndithudi mwapulumutsidwa kudzera m’chikhulupiriro,+ osati mwa inu nokha,+ koma monga mphatso ya Mulungu.+ Aefeso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:8 Mawu a Mulungu, ptsa. 91-92 Kukambitsirana, tsa. 97
8 Mwa kukoma mtima kwakukulu kumeneku, ndithudi mwapulumutsidwa kudzera m’chikhulupiriro,+ osati mwa inu nokha,+ koma monga mphatso ya Mulungu.+