-
Afilipi 3:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Zoonadi, ndimaona zinthu zonse kukhala zosapindulitsa, chifukwa chakuti ndinadziwa Khristu Yesu Ambuye wanga, chimene ndi chinthu chamtengo wapatali kwambiri.+ Chifukwa cha iye, ndimaona zinthu zonse kukhala zosapindulitsa, ndipo ndimaziyesa mulu wa zinyalala,+ kuti ndikhale pa ubwenzi weniweni ndi Khristu.
-