Afilipi 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Amenewo mapeto awo ndi chiwonongeko,+ ndipo mulungu wawo ndi mimba yawo.+ Ulemerero wawo uli m’zinthu zawo zochititsa manyazi,+ ndipo maganizo awo ali pa zinthu za dziko lapansi.+ Afilipi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:19 Nsanja ya Olonda,4/15/2008, ptsa. 4-56/15/2001, tsa. 1512/1/1990, ptsa. 4-5
19 Amenewo mapeto awo ndi chiwonongeko,+ ndipo mulungu wawo ndi mimba yawo.+ Ulemerero wawo uli m’zinthu zawo zochititsa manyazi,+ ndipo maganizo awo ali pa zinthu za dziko lapansi.+